2 Mbiri 36:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho anawabweretsera mfumu ya Akasidi+ yomwe inapha anyamata awo ndi lupanga+ mʼnyumba yopatulika.+ Sinamvere chisoni mnyamata kapena namwali, wachikulire kapena wodwala.+ Mulungu anapereka zonse mʼmanja mwake.+ Yeremiya 50:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu a ku Isiraeli ali ngati nkhosa zomwazikana.+ Mikango ndi imene yawabalalitsa.+ Poyamba, mfumu ya Asuri inawadya.+ Kenako Mfumu Nebukadinezara* ya ku Babulo inakukuta mafupa awo.+
17 Choncho anawabweretsera mfumu ya Akasidi+ yomwe inapha anyamata awo ndi lupanga+ mʼnyumba yopatulika.+ Sinamvere chisoni mnyamata kapena namwali, wachikulire kapena wodwala.+ Mulungu anapereka zonse mʼmanja mwake.+
17 Anthu a ku Isiraeli ali ngati nkhosa zomwazikana.+ Mikango ndi imene yawabalalitsa.+ Poyamba, mfumu ya Asuri inawadya.+ Kenako Mfumu Nebukadinezara* ya ku Babulo inakukuta mafupa awo.+