Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 2 Mbiri 20:5, 6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Kenako Yehosafati anaimirira pamaso pa gulu la anthu a ku Yuda ndi Yerusalemu, mʼnyumba ya Yehova patsogolo pa bwalo latsopano 6 nʼkunena kuti:

      “Inu Yehova Mulungu wa makolo athu, kodi si inu Mulungu wakumwamba?+ Kodi inu simukulamulira maufumu onse a mitundu ya anthu?+ Mʼdzanja lanu muli mphamvu ndipo palibe amene angalimbane nanu.+

  • Yesaya 43:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “Komanso, nthawi zonse ine sindisintha.+

      Ndipo palibe amene angathe kulanda chinthu chilichonse mʼdzanja langa.+

      Ndikachita chinthu, ndi ndani amene angaletse?”+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani