Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Deuteronomo 10:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Iye amachitira chilungamo ana amasiye ndi akazi amasiye,+ ndipo amakonda mlendo+ moti amamupatsa chakudya ndi zovala.

  • Yeremiya 22:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Yehova wanena kuti: “Muzichita zinthu motsatira malamulo komanso mwachilungamo. Muzipulumutsa munthu amene akuberedwa mʼmanja mwa munthu wakuba mwachinyengo. Musamachitire nkhanza mlendo aliyense amene akukhala mʼdziko lanu ndipo musamavulaze mwana wamasiye kapena mkazi wamasiye.+ Musamakhetse magazi a munthu aliyense wosalakwa mumzinda uno.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani