-
Yeremiya 25:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Choncho ndinatenga kapu imene inali mʼdzanja la Yehova ndipo ndinamwetsa mitundu yonse imene Yehova ananditumizako. Mitunduyo ndi iyi:+
-
-
Yeremiya 25:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Kenako ndinamwetsanso Farao mfumu ya Iguputo, atumiki ake, akalonga ake ndi anthu ake onse+
-
-
Ezekieli 29:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 “Iwe mwana wa munthu, yangʼana kwa Farao mfumu ya Iguputo ndipo ulosere zoipa zimene zidzachitikire iyeyo ndi dziko lonse la Iguputo.+
-