-
Yesaya 19:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ndidzapereka Iguputo mʼmanja mwa mbuye wankhanza
Ndipo mfumu yankhanza idzawalamulira,”+ akutero Ambuye woona, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
-