Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Ezekieli 26:8, 9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Anthu omwe akukhala mʼmidzi yako imene ili kunja kwa mzindawu adzawapha ndi lupanga. Iye adzamanga mpanda womenyerapo nkhondo komanso malo okwera omenyerapo nkhondo kuti amenyane nawe ndipo adzakuukira ndi chishango chachikulu. 9 Mfumuyo idzagumula mpanda wako ndi chida chogumulira,* ndipo idzagwetsa nsanja zako pogwiritsa ntchito nkhwangwa zake.*

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani