Yesaya 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Uwu ndi uthenga wokhudza Turo:+ Lirani mofuula inu sitima zapamadzi za ku Tarisi,+ Chifukwa chakuti doko lawonongedwa ndipo simungathenso kufikapo. Anthu amva zimenezi ali kudziko la Kitimu.+
23 Uwu ndi uthenga wokhudza Turo:+ Lirani mofuula inu sitima zapamadzi za ku Tarisi,+ Chifukwa chakuti doko lawonongedwa ndipo simungathenso kufikapo. Anthu amva zimenezi ali kudziko la Kitimu.+