Levitiko 26:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Mizinda yanu ndidzaiwononga+ ndi lupanga ndipo malo anu opatulika adzakhala opanda anthu, komanso sindidzalandira nsembe zanu za kafungo kosangalatsa.* Deuteronomo 29:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho Yehova anawazula mʼdziko lawo atapsa mtima,+ ali ndi ukali ndiponso mkwiyo waukulu nʼkuwapititsa kudziko lina, kumene ali lero.’+
31 Mizinda yanu ndidzaiwononga+ ndi lupanga ndipo malo anu opatulika adzakhala opanda anthu, komanso sindidzalandira nsembe zanu za kafungo kosangalatsa.*
28 Choncho Yehova anawazula mʼdziko lawo atapsa mtima,+ ali ndi ukali ndiponso mkwiyo waukulu nʼkuwapititsa kudziko lina, kumene ali lero.’+