-
Yesaya 41:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 “Taona! Ndakusandutsa chopunthira mbewu,+
Chida chatsopano chopunthira mbewu chokhala ndi mano akuthwa konsekonse.
Udzapondaponda mapiri nʼkuwaphwanya
Ndipo zitunda udzazisandutsa mankhusu.
-