Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yesaya 31:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Tsoka kwa anthu amene amapita ku Iguputo kukapempha thandizo,+

      Amene amadalira mahatchi,+

      Amene amadalira magaleta ankhondo chifukwa chakuti ndi ambiri,

      Komanso mahatchi ankhondo* chifukwa chakuti ndi amphamvu kwambiri.

      Koma sayangʼana kwa Woyera wa Isiraeli,

      Ndipo safunafuna Yehova.

  • Ezekieli 29:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Choncho anthu onse amene akukhala ku Iguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova,

      Chifukwa sanalinso ngati ndodo yothandiza nyumba ya Isiraeli poyenda, koma anali ngati tsekera.*+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani