-
Yesaya 31:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Koma Aiguputowo ndi anthu wamba ndipo si Mulungu.
Mahatchi awo ndi zinyama, osati mzimu.+
Yehova akadzatambasula dzanja lake,
Aliyense amene amapereka thandizo adzapunthwa
Ndipo aliyense amene akuthandizidwa adzagwa.
Onsewo adzawonongedwa nthawi imodzi.
-
-
Yeremiya 2:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Nʼchifukwa chiyani ukuona mopepuka kusakhulupirika kwako?
-