Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Deuteronomo 31:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Ineyo ndikudziwa bwino khalidwe lanu lopanduka+ ndi kuuma mtima* kwanu.+ Ngati mwakhala mukupandukira Yehova pamene ndili moyo, ndiye kuli bwanji pambuyo pa imfa yanga!

  • Yesaya 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Tsoka kwa mtundu wochimwa,+

      Anthu olemedwa ndi zolakwa,

      Ana a anthu ochita zoipa, ana a makhalidwe oipa.

      Iwo asiya Yehova.+

      Achitira Woyera wa Isiraeli zinthu zopanda ulemu.

      Iwo atembenuka nʼkumusiya.

  • Yeremiya 44:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Izi zinachitika chifukwa cha zinthu zoipa zimene ankachita nʼkundikhumudwitsa nazo. Iwo ankapitiriza kupereka nsembe+ ndi kutumikira milungu ina imene inuyo, iwowo kapena makolo anu simunkaidziwa.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani