Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yeremiya 13:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Zimenezi ndi zimene zidzakuchitikire. Limeneli ndi gawo limene ndakupatsa,” akutero Yehova,

      “Chifukwa chakuti wandiiwala+ ndipo ukukhulupirira zinthu zabodza.+

  • Mika 3:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Atsogoleri amumzindawo saweruza asanalandire ziphuphu,+

      Ansembe ake amaphunzitsa kuti apeze malipiro,+

      Ndipo aneneri ake amalosera kuti apeze ndalama.+

      Komatu iwo amanena kuti amadalira Yehova ndipo amati:

      “Yehovatu ali nafe,+

      Ndipo tsoka silidzatigwera.”+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani