-
1 Mbiri 5:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Pa nkhondoyo, Mulungu anawathandiza moti mbadwa za Hagara ndi onse amene anali nawo anaperekedwa mʼmanja mwawo popeza anapempha Mulunguyo kuti awathandize ndipo iye anamva kupembedzera kwawo chifukwa anamʼkhulupirira.+
-