Levitiko 26:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Deuteronomo 32:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kodi munthu mmodzi angathamangitse bwanji anthu 1,000,Kapena anthu awiri angathamangitse bwanji anthu 10,000?+ Nʼzosatheka, pokhapokha Thanthwe lawo litawagulitsa,+Komanso ngati Yehova atawapereka.
30 Kodi munthu mmodzi angathamangitse bwanji anthu 1,000,Kapena anthu awiri angathamangitse bwanji anthu 10,000?+ Nʼzosatheka, pokhapokha Thanthwe lawo litawagulitsa,+Komanso ngati Yehova atawapereka.