-
Yeremiya 31:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Chifukwa tsiku lidzafika limene alonda amene ali mʼmapiri a Efuraimu adzafuula kuti:
‘Nyamukani, tiyeni tipite ku Ziyoni kwa Yehova Mulungu wathu.’”+
-