Hoseya 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Efuraimu adzanena kuti, ‘Mafano alibenso ntchito kwa ine.’+ Ine ndidzamva ndipo ndidzamuyangʼanira.+ Ndidzakhala ngati mtengo wa mkungudza wobiriwira bwino. Ndipo mudzapeza zipatso kwa ine.” Zekariya 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, “Pa tsiku limenelo, ndidzafufuta mayina a mafano mʼdziko lonseli+ ndipo sadzakumbukiridwanso. Ndidzachotsamo aneneri+ komanso mzimu wonyansa.
8 Efuraimu adzanena kuti, ‘Mafano alibenso ntchito kwa ine.’+ Ine ndidzamva ndipo ndidzamuyangʼanira.+ Ndidzakhala ngati mtengo wa mkungudza wobiriwira bwino. Ndipo mudzapeza zipatso kwa ine.”
2 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, “Pa tsiku limenelo, ndidzafufuta mayina a mafano mʼdziko lonseli+ ndipo sadzakumbukiridwanso. Ndidzachotsamo aneneri+ komanso mzimu wonyansa.