-
Zekariya 10:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 “Pemphani Yehova kuti akugwetsereni mvula pa nthawi ya mvula yomalizira.
Yehova ndi amene amapanga mitambo yamvula,
Ndiponso amene amagwetsera anthu mvula.+
Iye amakulitsa mbewu mʼmunda mwa munthu aliyense.
-