-
Yesaya 3:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Yehova wanena kuti: “Chifukwa chakuti ana aakazi a Ziyoni ndi onyada,
Akuyenda mwamatama,*
Amakopa amuna ndi maso awo, nʼkumayenda modzigomera,
Komanso amapanga phokoso chifukwa cha zodzikongoletsera zimene amavala mʼmiyendo yawo,
-