-
Yesaya 22:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Iwe unali mzinda wodzaza ndi chipwirikiti,
Mzinda waphokoso komanso tauni yonyada.
Anthu ako amene aphedwa, sanaphedwe ndi lupanga
Kapena kufera kunkhondo.+
-