Yesaya 60:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mʼdziko lako simudzamvekanso zachiwawaMʼdziko lako simudzakhalanso kusakaza kapena kuwononga.+ Mipanda yako udzaitcha Chipulumutso+ ndipo mageti ako udzawatcha Tamanda. Yesaya 65:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yeremiya 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mʼmasiku a mfumu imeneyi, Yuda adzapulumutsidwa+ ndipo Isiraeli adzakhala motetezeka.+ Dzina la mfumuyi lidzakhala: Yehova Ndi Chilungamo Chathu.”+ Ezekieli 34:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ine ndidzachita pangano lamtendere ndi nkhosazo.+ Ndipo ndidzachotsa zilombo zolusa mʼdzikomo+ nʼcholinga choti nkhosazo zizidzakhala mʼchipululu zili zotetezeka ndipo zizidzagona munkhalango.+ Hoseya 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
18 Mʼdziko lako simudzamvekanso zachiwawaMʼdziko lako simudzakhalanso kusakaza kapena kuwononga.+ Mipanda yako udzaitcha Chipulumutso+ ndipo mageti ako udzawatcha Tamanda.
6 Mʼmasiku a mfumu imeneyi, Yuda adzapulumutsidwa+ ndipo Isiraeli adzakhala motetezeka.+ Dzina la mfumuyi lidzakhala: Yehova Ndi Chilungamo Chathu.”+
25 Ine ndidzachita pangano lamtendere ndi nkhosazo.+ Ndipo ndidzachotsa zilombo zolusa mʼdzikomo+ nʼcholinga choti nkhosazo zizidzakhala mʼchipululu zili zotetezeka ndipo zizidzagona munkhalango.+