Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Deuteronomo 28:66, 67
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 66 Moyo wanu udzakhala pangozi yaikulu koopsa, ndipo mudzakhala mwamantha usiku ndi masana, moti simudzakhala wotsimikiza ngati mudzakhalebe ndi moyo. 67 Mʼmawa mudzanena kuti, ‘Zikanakhala bwino akanakhala madzulo!’ ndipo madzulo mudzanena kuti, ‘Zikanakhala bwino ukanakhala mʼmawa!’ chifukwa cha mantha amene adzagwire mtima wanu, ndiponso chifukwa cha zimene maso anu adzaone.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani