-
Deuteronomo 7:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Yehova adzakuchotserani matenda onse ndipo sadzakugwetserani matenda alionse oopsa amene munawaona ku Iguputo.+ Koma adzawagwetsera pa anthu onse amene amadana nanu.
-