Yeremiya 51:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Wowononga adzafikira Babulo.+Asilikali ake adzagwidwa,+Mauta awo adzathyoledwa,Chifukwa Yehova ndi Mulungu amene amapereka chilango choyenera.+ Iye adzabwezera ndithu.+
56 Wowononga adzafikira Babulo.+Asilikali ake adzagwidwa,+Mauta awo adzathyoledwa,Chifukwa Yehova ndi Mulungu amene amapereka chilango choyenera.+ Iye adzabwezera ndithu.+