-
Deuteronomo 30:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ngakhale anthu a mtundu wanu amene anabalalitsidwawo atadzakhala kumalekezero kwa thambo, Yehova Mulungu wanu adzakusonkhanitsani nʼkukubweretsani kuchokera kumeneko.+
-