-
Yesaya 10:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Kodi zimene ndachitira Samariya ndi milungu yake yopanda phindu,+
Si zimenenso ndidzachitire Yerusalemu ndi mafano ake?’
-