-
Danieli 9:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Choncho ndinayangʼana kwa Yehova Mulungu woona ndipo ndinapemphera momuchonderera, ndinasala kudya,+ ndinavala ziguduli komanso kudzithira phulusa.
-