2 Mafumu 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mwina Yehova Mulungu wanu amva mawu onse a Rabisake, amene mbuye wake mfumu ya Asuri yamutuma kuti adzanyoze Mulungu wamoyo.+ Ndipo amulanga chifukwa cha mawu amene Yehova Mulungu wanu wamva. Choncho inuyo mupemphere+ mʼmalo mwa anthu amene atsala.’” 2 Mafumu 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tcherani khutu lanu, inu Yehova, mumve.+ Tsegulani maso anu,+ inu Yehova, muone. Imvani mawu amene Senakeribu watumiza onyoza Mulungu wamoyo.
4 Mwina Yehova Mulungu wanu amva mawu onse a Rabisake, amene mbuye wake mfumu ya Asuri yamutuma kuti adzanyoze Mulungu wamoyo.+ Ndipo amulanga chifukwa cha mawu amene Yehova Mulungu wanu wamva. Choncho inuyo mupemphere+ mʼmalo mwa anthu amene atsala.’”
16 Tcherani khutu lanu, inu Yehova, mumve.+ Tsegulani maso anu,+ inu Yehova, muone. Imvani mawu amene Senakeribu watumiza onyoza Mulungu wamoyo.