Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 2 Mafumu 19:25, 26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Kodi sunamve? Ndinakonza kalekale zimene ndidzachite.+

      Ndinakonza zimenezi mʼmasiku amakedzana.+

      Tsopano ndizichita.+

      Iweyo udzasandutsa mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri kukhala milu ya mabwinja.+

      26 Anthu okhala mʼmizindayo adzafooka.

      Adzachita mantha ndiponso adzachititsidwa manyazi.

      Adzakhala ngati zomera zakutchire komanso ngati udzu wanthete wobiriwira,+

      Ngati udzu womera padenga umene wawauka ndi mphepo yotentha yakumʼmawa.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani