-
Yesaya 1:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba akanapanda kutisiyira anthu ochepa opulumuka,
Tikanakhala ngati Sodomu,
Ndipo tikanafanana ndi Gomora.+
-