32 Choncho Yehova wanena izi zokhudza mfumu ya Asuri:+
“Sadzalowa mumzindawu+
Kapena kuponyamo muvi
Kapena kufikamo ndi chishango
Kapenanso kumanga malo okwera omenyerapo nkhondo atauzungulira.+
33 Adzabwerera kudzera njira imene anadutsa pobwera,
Ndipo sadzalowa mumzindawu.” Watero Yehova.
34 “Ndidzateteza mzindawu+ ndipo ndidzaupulumutsa chifukwa cha ineyo+
Ndiponso chifukwa cha mtumiki wanga Davide.”’”+