-
Yesaya 31:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Mofanana ndi mbalame imene imauluka kuti iteteze ana ake, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba adzateteza mzinda wa Yerusalemu.+
Iye adzauteteza nʼkuupulumutsa.
Adzaonetsetsa kuti usawonongedwe ndipo adzaulanditsa.”
-