-
2 Mafumu 20:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Hezekiya anali atafunsa Yesaya kuti: “Kodi chizindikiro+ chakuti Yehova andichiritsa ndipo ndidzapitadi kunyumba ya Yehova pa tsiku lachitatu nʼchiyani?”
-