Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yesaya 48:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Ayi, inu simunamve+ kapena kudziwa zimenezi,

      Ndipo mʼmbuyomu makutu anu anali osatseguka,

      Chifukwa ndikudziwa kuti inu ndi achinyengo,+

      Ndipo kuyambira pamene munabadwa mumatchedwa wochimwa.+

  • Hoseya 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kenako Yehova anandiuza kuti: “Pita ukayambenso kukonda mkazi amene akukondedwa ndi mwamuna wina ndipo akuchita chigololo.+ Ukamukonde ngati mmene Yehova amakondera Aisiraeli,+ ngakhale kuti iwo amalambira milungu ina+ komanso amakonda makeke a mphesa.”*

  • Hoseya 5:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Akhala osakhulupirika kwa Yehova,+

      Chifukwa abereka ana achilendo.

      Tsopano mwezi udzawadya* limodzi ndi zinthu zawo.*

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani