-
Yeremiya 38:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 “Inu mbuyanga mfumu, zimene anthu awa achitira mneneri Yeremiya ndi zoipa. Iwo amuponya mʼchitsime ndipo afera momwemo chifukwa cha njala, popeza mkate watheratu mumzindawu.”+
-