-
2 Mafumu 25:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Gedaliya analumbirira akuluakuluwo ndi asilikali awo kuti: “Musaope kukhala atumiki a Akasidi. Khalani mʼdzikoli nʼkumatumikira mfumu ya Babulo ndipo zinthu zikuyenderani bwino.”+
-
-
Yeremiya 27:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Koma mtundu wa anthu umene udzaike khosi lake mʼgoli la mfumu ya Babulo nʼkuitumikira, ndidzaulola kuti ukhalebe* mʼdziko lawo ndipo udzalima minda nʼkumakhala mʼdzikolo,’ akutero Yehova.”’”
-