Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 1 Mafumu 15:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndiyeno Mfumu Asa inaitanitsa Ayuda onse moti palibe amene anatsala, ndipo iwo anatenga miyala ndi matabwa za ku Rama zimene Basa ankamangira. Mfumu Asa anatenga zinthu zimenezi nʼkukamangira mzinda wa Geba+ ku Benjamini ndi wa Mizipa+ kuti mizindayi ikhale yolimba.

  • 2 Mbiri 16:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno Mfumu Asa inatenga Ayuda onse nʼkupita kukatenga miyala ndi matabwa za ku Rama+ zimene Basa ankamangira+ ndipo anakamangira mzinda wa Geba+ ndi wa Mizipa+ kuti mizindayi ikhale yolimba.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani