-
Yeremiya 42:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 ponena kuti, “Ayi, mʼmalomwake tipita kudziko la Iguputo,+ kumene sitidzaona nkhondo kapena kumva kulira kwa lipenga komanso kumene sitidzasowa chakudya. Ife tizikakhala kumeneko,”
-
-
Yeremiya 43:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Iwo anapita mʼdziko la Iguputo chifukwa sanamvere mawu a Yehova ndipo anakafika ku Tahapanesi.+
-