Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yeremiya 40:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Nayenso Yohanani mwana wa Kareya ndi akuluakulu onse a asilikali amene anali mʼdziko lonselo, anabwera kwa Gedaliya ku Mizipa. 14 Iwo anauza Gedaliya kuti: “Kodi sukudziwa kuti Baalisi mfumu ya a Amoni,+ watumiza Isimaeli mwana wa Netaniya kuti adzakuphe?”+ Koma Gedaliya mwana wa Ahikamu sanawakhulupirire.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani