-
2 Mbiri 24:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Yehova anapitiriza kuwatumizira aneneri kuti awathandize kubwerera kwa iye. Aneneriwo anapitiriza kuwachenjeza, koma sanamvere.+
-