Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yeremiya 36:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiyeno Yeremiya anaitana Baruki+ mwana wa Neriya nʼkumuuza mawu onse amene Yehova anamuuza ndipo Baruki analemba mawuwo mumpukutu.+

  • Yeremiya 36:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Kenako Yeremiya anatenga mpukutu wina nʼkupatsa Baruki mlembi,+ mwana wa Neriya. Baruki analembamo mawu onse amene Yeremiya anamuuza, amene anali mumpukutu umene Yehoyakimu mfumu ya Yuda inawotcha.+ Mumpukutumo anawonjezeramo mawu ena ambiri ochokera kwa Mulungu.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani