-
Ezekieli 30:4, 5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Lupanga lidzabwera kudzaukira Iguputo, ndipo anthu a ku Itiyopiya adzachita mantha kwambiri anthu akadzaphedwa ku Iguputo.
Chuma cha Iguputo chidzalandidwa ndipo maziko ake adzagwetsedwa.+
-