-
Ezekieli 32:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 ‘Ndidzachititsa kuti mitima ya anthu ambiri ikhale ndi nkhawa ndikadzatenga anthu ako ogwidwa ukapolo nʼkuwapititsa kwa anthu a mitundu ina,
Kumayiko amene sukuwadziwa.+
-