-
Yeremiya 16:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 ‘Anthu amʼdzikoli adzafa, kaya ndi olemekezeka kapena onyozeka.
Sadzaikidwa mʼmanda,
Palibe aliyense amene adzalire maliro awo,
Kapena kudzichekacheka komanso kumeta mpala chifukwa cha iwo.*
-