-
Yeremiya 8:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Mahatchi ake akumveka kupuma mwawefuwefu ali ku Dani.
Dziko lonse lagwedezeka
Chifukwa cha phokoso la kumemesa* kwa mahatchi ake amphongo.
Adani akubwera kudzawononga dziko ndi chilichonse chimene chili mmenemo,
Mzinda ndi anthu okhala mmenemo.”
-