1 Mafumu 12:28, 29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Hoseya 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu anthu a ku Beteli, wina adzakuchitaninso zimenezi+ chifukwa ndinu oipa kwambiri. Ndithu, mfumu ya Isiraeli idzawonongedwa* mʼbandakucha.”+ Amosi 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Musakhale ndi mtima wofuna kupita ku Beteli.+Ndipo musapite ku Giligala+ kapena ku Beere-seba.+Chifukwa ndithu Giligala adzapita ku ukapolo.+Ndipo Beteli adzawonongedwa.*
15 Inu anthu a ku Beteli, wina adzakuchitaninso zimenezi+ chifukwa ndinu oipa kwambiri. Ndithu, mfumu ya Isiraeli idzawonongedwa* mʼbandakucha.”+
5 Musakhale ndi mtima wofuna kupita ku Beteli.+Ndipo musapite ku Giligala+ kapena ku Beere-seba.+Chifukwa ndithu Giligala adzapita ku ukapolo.+Ndipo Beteli adzawonongedwa.*