Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Numeri 21:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Tiyeni tiwalase.

      Hesiboni adzawonongedwa mpaka ku Diboni.+

      Tiyeni timusandutse bwinja mpaka ku Nofa,

      Moto udzafalikira mpaka ku Medeba.”+

  • Yoswa 13:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kenako Mose anagawira cholowa fuko la Rubeni motsatira mabanja awo.

  • Yoswa 13:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Linafikanso ku Hesiboni ndi midzi yake yonse+ imene inali mʼmalo okwera, ku Diboni, ku Bamoti-baala komanso ku Beti-baala-meoni.+

  • Yesaya 15:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Iye wapita kukachisi ndi ku Diboni,+

      Wapita kumalo okwezeka kukalira.

      Mowabu akulira mofuula chifukwa cha zimene zachitikira Nebo+ ndi Medeba.+

      Mutu uliwonse aumeta mpala+ ndipo ndevu zonse zametedwa.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani