-
Maliro 4:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Anthu amene ankatithamangitsa anali aliwiro kuposa ziwombankhanga zouluka mʼmwamba.+
Iwo anatithamangitsa mʼmapiri. Anatibisalira mʼchipululu.
-
-
Habakuku 1:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Mahatchi ake ankhondo amathamanga kwambiri.
Mahatchi awo amachokera kutali.
Ndipo amauluka ngati chiwombankhanga chimene chikuthamanga kuti chikapeze chakudya.+
-