Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Genesis 36:10, 11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Ezekieli 25:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Nditambasulanso dzanja langa nʼkulanga Edomu ndipo ndipha anthu ndi ziweto mʼdzikolo, moti ndidzalisandutsa bwinja.+ Anthu adzaphedwa ndi lupanga kuyambira ku Temani mpaka ku Dedani.+

  • Amosi 1:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Choncho ndidzatumiza moto ku Temani,+

      Ndipo udzawotcheratu nsanja zolimba za ku Bozira.’+

  • Obadiya 8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Yehova akuti: “Kodi pa tsiku limenelo,

      Sindidzawononga anthu anzeru mu Edomu,+

      Komanso anthu ozindikira mʼdera lamapiri la Esau?

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani