Yesaya 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzachititsa Amedi kuti awaukire,+Amene saona siliva ngati kanthuNdipo sasangalala ndi golide. Yeremiya 51:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Nolani mivi yanu.*+ Tengani zishango zozungulira. Yehova walimbikitsa* mafumu a Amedi kuti akamenye nkhondo,+Chifukwa akufuna kuwononga Babulo. Yehova akubwezera Babulo, akumubwezera chifukwa cha kachisi wake. Yeremiya 51:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Kumwamba ndi dziko lapansi komanso chilichonse cha mmenemoZidzafuula mosangalala poona kuti Babulo wagwa,+Chifukwa owononga adzabwera kwa iye kuchokera kumpoto,”+ akutero Yehova.
11 “Nolani mivi yanu.*+ Tengani zishango zozungulira. Yehova walimbikitsa* mafumu a Amedi kuti akamenye nkhondo,+Chifukwa akufuna kuwononga Babulo. Yehova akubwezera Babulo, akumubwezera chifukwa cha kachisi wake.
48 Kumwamba ndi dziko lapansi komanso chilichonse cha mmenemoZidzafuula mosangalala poona kuti Babulo wagwa,+Chifukwa owononga adzabwera kwa iye kuchokera kumpoto,”+ akutero Yehova.